×

Ndipo mawu awo asakukhumudwitse iwe. Ndithudi mphamvu zonse Mwini wake ndi Mulungu. 10:65 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yunus ⮕ (10:65) ayat 65 in Chichewa

10:65 Surah Yunus ayat 65 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 65 - يُونس - Page - Juz 11

﴿وَلَا يَحۡزُنكَ قَوۡلُهُمۡۘ إِنَّ ٱلۡعِزَّةَ لِلَّهِ جَمِيعًاۚ هُوَ ٱلسَّمِيعُ ٱلۡعَلِيمُ ﴾
[يُونس: 65]

Ndipo mawu awo asakukhumudwitse iwe. Ndithudi mphamvu zonse Mwini wake ndi Mulungu. Iye ndi wakumva ndi wodziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا يحزنك قولهم إن العزة لله جميعا هو السميع العليم, باللغة نيانجا

﴿ولا يحزنك قولهم إن العزة لله جميعا هو السميع العليم﴾ [يُونس: 65]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (iwe, Mtumiki) zisakudandaulitse zonena zawo (zomwe akukunenera monyoza). Ndithu ulemelero ndi mphamvu zonse nza Allah. Iye Ngwakumva, Ngodziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek