×

Chimenecho ndicho chilango cha Ambuye wako akafuna kulanga mzinda wa anthu ochita 11:102 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Hud ⮕ (11:102) ayat 102 in Chichewa

11:102 Surah Hud ayat 102 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 102 - هُود - Page - Juz 12

﴿وَكَذَٰلِكَ أَخۡذُ رَبِّكَ إِذَآ أَخَذَ ٱلۡقُرَىٰ وَهِيَ ظَٰلِمَةٌۚ إِنَّ أَخۡذَهُۥٓ أَلِيمٞ شَدِيدٌ ﴾
[هُود: 102]

Chimenecho ndicho chilango cha Ambuye wako akafuna kulanga mzinda wa anthu ochita zoipa. Ndithudi chilango chake ndi chokhwima ndi chowawa kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وكذلك أخذ ربك إذا أخذ القرى وهي ظالمة إن أخذه أليم شديد, باللغة نيانجا

﴿وكذلك أخذ ربك إذا أخذ القرى وهي ظالمة إن أخذه أليم شديد﴾ [هُود: 102]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mmenemo ndi momwe kumakhalira kulanga kwa Mbuye wako pamene alanga anthu a m’mizinda akakhala oipa (pa makhalidwe). Ndithu kulanga kwake (Allah) nkowawa, nkwaukali
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek