Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 104 - هُود - Page - Juz 12
﴿وَمَا نُؤَخِّرُهُۥٓ إِلَّا لِأَجَلٖ مَّعۡدُودٖ ﴾
[هُود: 104]
﴿وما نؤخره إلا لأجل معدود﴾ [هُود: 104]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo sitikulichedwetsa koma m’nthawi yowerengeka (kwa Allah, ngakhale kuti kwa anthu likuoneka kuti lili kutali) |