×

Kuti musapembedze wina aliyense koma Mulungu. Ndithudi ine ndine wochokera kwa Iye 11:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Hud ⮕ (11:2) ayat 2 in Chichewa

11:2 Surah Hud ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 2 - هُود - Page - Juz 11

﴿أَلَّا تَعۡبُدُوٓاْ إِلَّا ٱللَّهَۚ إِنَّنِي لَكُم مِّنۡهُ نَذِيرٞ وَبَشِيرٞ ﴾
[هُود: 2]

Kuti musapembedze wina aliyense koma Mulungu. Ndithudi ine ndine wochokera kwa Iye wochenjeza ndi wobweretsa nkhani zabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألا تعبدوا إلا الله إنني لكم منه نذير وبشير, باللغة نيانجا

﴿ألا تعبدوا إلا الله إنني لكم منه نذير وبشير﴾ [هُود: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“(Wachita zimenezi) kuti musampembedze wina wake koma Allah yekha. Ndithudi ine kwa inu ndimchenjezi wochokera kwa Iye ndiponso wokuuzani nkhani zabwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek