×

“Anthu anga! Kwaniritsani muyeso wa zinthu ndipo yesani mwachilungamo ndipo musawapungulire anthu 11:85 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Hud ⮕ (11:85) ayat 85 in Chichewa

11:85 Surah Hud ayat 85 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 85 - هُود - Page - Juz 12

﴿وَيَٰقَوۡمِ أَوۡفُواْ ٱلۡمِكۡيَالَ وَٱلۡمِيزَانَ بِٱلۡقِسۡطِۖ وَلَا تَبۡخَسُواْ ٱلنَّاسَ أَشۡيَآءَهُمۡ وَلَا تَعۡثَوۡاْ فِي ٱلۡأَرۡضِ مُفۡسِدِينَ ﴾
[هُود: 85]

“Anthu anga! Kwaniritsani muyeso wa zinthu ndipo yesani mwachilungamo ndipo musawapungulire anthu katundu wawo ndipo musachite zoipa padziko ndikuyambitsa chisokonezo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وياقوم أوفوا المكيال والميزان بالقسط ولا تبخسوا الناس أشياءهم ولا تعثوا في, باللغة نيانجا

﴿وياقوم أوفوا المكيال والميزان بالقسط ولا تبخسوا الناس أشياءهم ولا تعثوا في﴾ [هُود: 85]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipo E inu anthu anga! Kwaniritsani mulingo wa mbale ndi wasikelo mwachilungamo, ndipo musawachepetsere anthu zinthu zawo (mwachinyengo). Ndipo musafalitse zoipa pa dziko ndi cholinga chodzetsa chisokonezo.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek