Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 9 - هُود - Page - Juz 12
﴿وَلَئِنۡ أَذَقۡنَا ٱلۡإِنسَٰنَ مِنَّا رَحۡمَةٗ ثُمَّ نَزَعۡنَٰهَا مِنۡهُ إِنَّهُۥ لَيَـُٔوسٞ كَفُورٞ ﴾
[هُود: 9]
﴿ولئن أذقنا الإنسان منا رحمة ثم نـزعناها منه إنه ليئوس كفور﴾ [هُود: 9]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo munthu tikamulawitsa mtendere wochokera kwa Ife, kenako nkuuchotsa kwa iye, ndithu amakhala wotaya mtima kwambiri ndikukhala wosathokoza |