×

“Ambuye, Inu ndithudi, mwandipatsa ine ulemerero ndi kundiphunzitsa kutanthauzira maloto. Inu ndinu 12:101 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:101) ayat 101 in Chichewa

12:101 Surah Yusuf ayat 101 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 101 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿۞ رَبِّ قَدۡ ءَاتَيۡتَنِي مِنَ ٱلۡمُلۡكِ وَعَلَّمۡتَنِي مِن تَأۡوِيلِ ٱلۡأَحَادِيثِۚ فَاطِرَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ أَنتَ وَلِيِّۦ فِي ٱلدُّنۡيَا وَٱلۡأٓخِرَةِۖ تَوَفَّنِي مُسۡلِمٗا وَأَلۡحِقۡنِي بِٱلصَّٰلِحِينَ ﴾
[يُوسُف: 101]

“Ambuye, Inu ndithudi, mwandipatsa ine ulemerero ndi kundiphunzitsa kutanthauzira maloto. Inu ndinu Namalenga wakumwamba ndi dziko lapansi. Inu ndinu Msungi wanga m’dziko lino ndiponso m’dziko limene lili nkudza. Ndilekeni kuti ndife ndili kukulambirani inu ndipo ndiikeni m’gulu la anthu abwino.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: رب قد آتيتني من الملك وعلمتني من تأويل الأحاديث فاطر السموات والأرض, باللغة نيانجا

﴿رب قد آتيتني من الملك وعلمتني من تأويل الأحاديث فاطر السموات والأرض﴾ [يُوسُف: 101]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kenako adathokoza ndi kupempha Allah kuti): “E Mbuye wanga! Ndithu mwandipatsako ufumu ndi kundiphunzitsako kumasulira nkhani (maloto). E Inu Mlengi wa thambo ndi nthaka! Inu ndiye Mtetezi wanga pa dziko lapansi ndi tsiku la chimaliziro. (Ndipo nthawi ya imfa yanga) mudzandipatse imfa ndili Msilamu ndipo kandikumanitseni ndi ochita zabwino.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek