Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 27 - يُوسُف - Page - Juz 12
﴿وَإِن كَانَ قَمِيصُهُۥ قُدَّ مِن دُبُرٖ فَكَذَبَتۡ وَهُوَ مِنَ ٱلصَّٰدِقِينَ ﴾
[يُوسُف: 27]
﴿وإن كان قميصه قد من دبر فكذبت وهو من الصادقين﴾ [يُوسُف: 27]
Khaled Ibrahim Betala ““Koma ngati mkanjo wake wang’ambidwa chakumbuyo ndiye kuti (mkazi uyu) wanena bodza ndipo iye (Yûsuf) ndi mmodzi mwa onena zoona.” |