Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 28 - يُوسُف - Page - Juz 12
﴿فَلَمَّا رَءَا قَمِيصَهُۥ قُدَّ مِن دُبُرٖ قَالَ إِنَّهُۥ مِن كَيۡدِكُنَّۖ إِنَّ كَيۡدَكُنَّ عَظِيمٞ ﴾
[يُوسُف: 28]
﴿فلما رأى قميصه قد من دبر قال إنه من كيدكن إن كيدكن﴾ [يُوسُف: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho (mwamuna uja) pamene adaona mkanjo wake (wa Yûsuf) utang’ambidwa chakumbuyo, (adadziwa kuti Yûsuf ndi amene amafuna kugwiliridwa), adati: “Ndithudi, izi ndi ndale zanu akazi. Ndithu ndale zanu ndi zazikulu (iwe mkazi wanga ndi amene udatsimikiza kuchita choipa ndi mnyamatayu).” |