×

Ndipo amai a mumzinda muja adati: “Mkazi wa Mfumu alikunyenga mnyamata wake. 12:30 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:30) ayat 30 in Chichewa

12:30 Surah Yusuf ayat 30 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 30 - يُوسُف - Page - Juz 12

﴿۞ وَقَالَ نِسۡوَةٞ فِي ٱلۡمَدِينَةِ ٱمۡرَأَتُ ٱلۡعَزِيزِ تُرَٰوِدُ فَتَىٰهَا عَن نَّفۡسِهِۦۖ قَدۡ شَغَفَهَا حُبًّاۖ إِنَّا لَنَرَىٰهَا فِي ضَلَٰلٖ مُّبِينٖ ﴾
[يُوسُف: 30]

Ndipo amai a mumzinda muja adati: “Mkazi wa Mfumu alikunyenga mnyamata wake. Ndithudi iye anali kumulakalaka zedi. Ndithudi ife tili kuona kuti mkaziyu wasochera kwambiri.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال نسوة في المدينة امرأة العزيز تراود فتاها عن نفسه قد شغفها, باللغة نيانجا

﴿وقال نسوة في المدينة امرأة العزيز تراود فتاها عن نفسه قد شغفها﴾ [يُوسُف: 30]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akazi a mu mzindamo (ataimva nkhaniyi) anati: “Mkazi wa nduna akulakalaka m’nyamata wake popanda kulakalakidwa ndi iye; ndithu chikondi chamufooketsa zedi; ndithudi, ife tikumuona (mkaziyu kuti) ali m’kusokera koonekera.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek