Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 58 - يُوسُف - Page - Juz 13
﴿وَجَآءَ إِخۡوَةُ يُوسُفَ فَدَخَلُواْ عَلَيۡهِ فَعَرَفَهُمۡ وَهُمۡ لَهُۥ مُنكِرُونَ ﴾
[يُوسُف: 58]
﴿وجاء إخوة يوسف فدخلوا عليه فعرفهم وهم له منكرون﴾ [يُوسُف: 58]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adadza abale (ake) a Yûsuf (kukafuna chakudya kumeneko pamene ku Kenani kudagwa chilala chadzaoneni) ndikulowa kwa iye, ndipo (iye) adawazindikira pomwe iwo sankamzindikira |