×

Ndipo pamene iye adawakonzera chakudya chawo, iye adati, “Ndibweretsereni m’bale wanu mwa 12:59 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:59) ayat 59 in Chichewa

12:59 Surah Yusuf ayat 59 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 59 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿وَلَمَّا جَهَّزَهُم بِجَهَازِهِمۡ قَالَ ٱئۡتُونِي بِأَخٖ لَّكُم مِّنۡ أَبِيكُمۡۚ أَلَا تَرَوۡنَ أَنِّيٓ أُوفِي ٱلۡكَيۡلَ وَأَنَا۠ خَيۡرُ ٱلۡمُنزِلِينَ ﴾
[يُوسُف: 59]

Ndipo pamene iye adawakonzera chakudya chawo, iye adati, “Ndibweretsereni m’bale wanu mwa abambo anu. Kodi inu simukuona kuti ine ndikukwaniritsa muyeso ndiponso ndimalandira bwino alendo?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولما جهزهم بجهازهم قال ائتوني بأخ لكم من أبيكم ألا ترون أني, باللغة نيانجا

﴿ولما جهزهم بجهازهم قال ائتوني بأخ لكم من أبيكم ألا ترون أني﴾ [يُوسُف: 59]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pamene adawakonzera chakudya chawo, adati: “(Ngatimudzabwereranso kachiwiri) mudzabwere ndi m‘bale wanu wa kumbali ya bambo anu, kodi simuona kuti ine ndikukwaniritsa muyeso, ndipo ndine wabwino kwambiri polandira (alendo)?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek