×

Yakobo adati, “Kodi ine ndikukhulupirireni pokupatsani uyu monga momwe ndidakukhulupirirani kale ndi 12:64 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:64) ayat 64 in Chichewa

12:64 Surah Yusuf ayat 64 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 64 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿قَالَ هَلۡ ءَامَنُكُمۡ عَلَيۡهِ إِلَّا كَمَآ أَمِنتُكُمۡ عَلَىٰٓ أَخِيهِ مِن قَبۡلُ فَٱللَّهُ خَيۡرٌ حَٰفِظٗاۖ وَهُوَ أَرۡحَمُ ٱلرَّٰحِمِينَ ﴾
[يُوسُف: 64]

Yakobo adati, “Kodi ine ndikukhulupirireni pokupatsani uyu monga momwe ndidakukhulupirirani kale ndi m’bale wake uja? Komatu Mulungu ndiye Msungi wabwino ndipo Iye ndiye wachifundo mwa achifundo onse.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال هل آمنكم عليه إلا كما أمنتكم على أخيه من قبل فالله, باللغة نيانجا

﴿قال هل آمنكم عليه إلا كما أمنتكم على أخيه من قبل فالله﴾ [يُوسُف: 64]

Khaled Ibrahim Betala
“(Ya’qub) adati: “Kodi ndingakukhulupirireni pa iye kuposa momwe ndidakukhulupirirani pa m’bale wake kale (yemwe mudamsokeretsa)? Koma Allah ndi Yemwe ali Wabwino posunga, Ndipo Iye Ngwachifundo zedi kuposa achifundo onse.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek