×

Iwo adati, “Tikusowa mbale ya Mfumu ndipo aliyense amene abweretse mbale adzalandira 12:72 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:72) ayat 72 in Chichewa

12:72 Surah Yusuf ayat 72 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 72 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿قَالُواْ نَفۡقِدُ صُوَاعَ ٱلۡمَلِكِ وَلِمَن جَآءَ بِهِۦ حِمۡلُ بَعِيرٖ وَأَنَا۠ بِهِۦ زَعِيمٞ ﴾
[يُوسُف: 72]

Iwo adati, “Tikusowa mbale ya Mfumu ndipo aliyense amene abweretse mbale adzalandira katundu wokwana kunyamula ndi ngamira imodzi. Ndipo ine ndine mboni.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا نفقد صواع الملك ولمن جاء به حمل بعير وأنا به زعيم, باللغة نيانجا

﴿قالوا نفقد صواع الملك ولمن جاء به حمل بعير وأنا به زعيم﴾ [يُوسُف: 72]

Khaled Ibrahim Betala
“Adati: “Tikusowa muyeso wa Mfumu; ndipo amene aubweretse, alandira mtolo wangamira yathunthu.” (Ndipo Mneneri Yûsuf adati): “Ndipo ine ndine muimiliri pa zimenezi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek