Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 12 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿هُوَ ٱلَّذِي يُرِيكُمُ ٱلۡبَرۡقَ خَوۡفٗا وَطَمَعٗا وَيُنشِئُ ٱلسَّحَابَ ٱلثِّقَالَ ﴾
[الرَّعد: 12]
﴿هو الذي يريكم البرق خوفا وطمعا وينشئ السحاب الثقال﴾ [الرَّعد: 12]
Khaled Ibrahim Betala “Iye ndi Yemwe amakuonetsani kung’anima mokuopyezani (kuphedwa ndi mphezi) ndi mokupatsani chiyembekezo chabwino (chakudza mvula). Ndipo amabweretsa mitambo yolemera (ndi madzi amvula) |