Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 8 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿ٱللَّهُ يَعۡلَمُ مَا تَحۡمِلُ كُلُّ أُنثَىٰ وَمَا تَغِيضُ ٱلۡأَرۡحَامُ وَمَا تَزۡدَادُۚ وَكُلُّ شَيۡءٍ عِندَهُۥ بِمِقۡدَارٍ ﴾
[الرَّعد: 8]
﴿الله يعلم ما تحمل كل أنثى وما تغيض الأرحام وما تزداد وكل﴾ [الرَّعد: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Allah akudziwa chilichonse chimene mkazi asenza (m’mimba mwake) ndi zimene mimba zikupungula ndi zimene zikuonjezera. Chinthu chilichonse kwa Iye chili ndi mlingo (wake) |