×

Mulungu adzalimbikitsa anthu okhulupirira ndi liwu lokhazikika m’moyo uno ndi m’moyo umene 14:27 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:27) ayat 27 in Chichewa

14:27 Surah Ibrahim ayat 27 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 27 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿يُثَبِّتُ ٱللَّهُ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ بِٱلۡقَوۡلِ ٱلثَّابِتِ فِي ٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَا وَفِي ٱلۡأٓخِرَةِۖ وَيُضِلُّ ٱللَّهُ ٱلظَّٰلِمِينَۚ وَيَفۡعَلُ ٱللَّهُ مَا يَشَآءُ ﴾
[إبراهِيم: 27]

Mulungu adzalimbikitsa anthu okhulupirira ndi liwu lokhazikika m’moyo uno ndi m’moyo umene uli nkudza. Ndipo Mulungu adzasocheretsa ochita zoipa ndipo Mulungu amachita zimene Iye afuna

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يثبت الله الذين آمنوا بالقول الثابت في الحياة الدنيا وفي الآخرة ويضل, باللغة نيانجا

﴿يثبت الله الذين آمنوا بالقول الثابت في الحياة الدنيا وفي الآخرة ويضل﴾ [إبراهِيم: 27]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah amawalimbikitsa amene akhulupirira ndi mawu olimba m’moyo wa dziko lapansi, ndi moyo wapambuyo pa imfa; ndipo Allah amawalekelera kusokera omwe akudzichitira okha zoipa; ndipo Allah amachita zimene wafuna
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek