Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 36 - إبراهِيم - Page - Juz 13
﴿رَبِّ إِنَّهُنَّ أَضۡلَلۡنَ كَثِيرٗا مِّنَ ٱلنَّاسِۖ فَمَن تَبِعَنِي فَإِنَّهُۥ مِنِّيۖ وَمَنۡ عَصَانِي فَإِنَّكَ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[إبراهِيم: 36]
﴿رب إنهن أضللن كثيرا من الناس فمن تبعني فإنه مني ومن عصاني﴾ [إبراهِيم: 36]
Khaled Ibrahim Betala ““Mbuye wanga! Ndithu (mafano) awa asokeretsa anthu ambiri. Choncho amene wanditsata, ndithu iyeyo ali mwa ine (mudzamulipira chabwino monga mwandilonjeza), ndipo amene wandinyoza (mutha kumukhululukira) ndithu Inu Ngokhululuka kwambiri, Ngwachisoni.” |