×

“Oh Ambuye wathu! Ine ndakhazika ena mwa ana anga m’dambo lopanda zomera 14:37 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:37) ayat 37 in Chichewa

14:37 Surah Ibrahim ayat 37 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 37 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿رَّبَّنَآ إِنِّيٓ أَسۡكَنتُ مِن ذُرِّيَّتِي بِوَادٍ غَيۡرِ ذِي زَرۡعٍ عِندَ بَيۡتِكَ ٱلۡمُحَرَّمِ رَبَّنَا لِيُقِيمُواْ ٱلصَّلَوٰةَ فَٱجۡعَلۡ أَفۡـِٔدَةٗ مِّنَ ٱلنَّاسِ تَهۡوِيٓ إِلَيۡهِمۡ وَٱرۡزُقۡهُم مِّنَ ٱلثَّمَرَٰتِ لَعَلَّهُمۡ يَشۡكُرُونَ ﴾
[إبراهِيم: 37]

“Oh Ambuye wathu! Ine ndakhazika ena mwa ana anga m’dambo lopanda zomera limene lili pafupi ndi Nyumba yanu yoyera, Oh Ambuye wathu, kuti iwo azipemphera. Motero dzazani mitima ya anthu ndi chikondi kuti awaonetsere iwo ndipo apatseni iwo zipatso kuti akhale othokoza.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ربنا إني أسكنت من ذريتي بواد غير ذي زرع عند بيتك المحرم, باللغة نيانجا

﴿ربنا إني أسكنت من ذريتي بواد غير ذي زرع عند بيتك المحرم﴾ [إبراهِيم: 37]

Khaled Ibrahim Betala
““Mbuye wanga! Ndithu ine ndaikhazika ina mwa mbumba yanga (mwana wanga Ismail) pachigwa ichi (cha Makka) chopanda zomera pa Nyumba Yanu Yopatulika (Al-Ka’ba); Mbuye wathu (aloleni) kuti akhale opemphera Swala; choncho ichiteni mitima ya anthu kukhala yopendekera kwa iwo (akonde kudzakhala malo amenewo), ndipo apatseni zipatso kuti athokoze.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek