Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 38 - إبراهِيم - Page - Juz 13
﴿رَبَّنَآ إِنَّكَ تَعۡلَمُ مَا نُخۡفِي وَمَا نُعۡلِنُۗ وَمَا يَخۡفَىٰ عَلَى ٱللَّهِ مِن شَيۡءٖ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَلَا فِي ٱلسَّمَآءِ ﴾
[إبراهِيم: 38]
﴿ربنا إنك تعلم ما نخفي وما نعلن وما يخفى على الله من﴾ [إبراهِيم: 38]
Khaled Ibrahim Betala ““Mbuye wathu! Ndithu Inu mukudziwa zimene tikubisa ndi zomwe tikuonetsa poyera. Ndipo palibe chilichonse chobisika kwa Allah, m’dziko kapena kumwamba |