×

Musaganize kuti Mulungu adzalephera kukwaniritsa lonjezo lake limene adapereka kwa Atumwi ake. 14:47 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:47) ayat 47 in Chichewa

14:47 Surah Ibrahim ayat 47 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 47 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿فَلَا تَحۡسَبَنَّ ٱللَّهَ مُخۡلِفَ وَعۡدِهِۦ رُسُلَهُۥٓۚ إِنَّ ٱللَّهَ عَزِيزٞ ذُو ٱنتِقَامٖ ﴾
[إبراهِيم: 47]

Musaganize kuti Mulungu adzalephera kukwaniritsa lonjezo lake limene adapereka kwa Atumwi ake. Ndithudi Mulungu ali ndi mphamvu ndipo amatha kulanga

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فلا تحسبن الله مخلف وعده رسله إن الله عزيز ذو انتقام, باللغة نيانجا

﴿فلا تحسبن الله مخلف وعده رسله إن الله عزيز ذو انتقام﴾ [إبراهِيم: 47]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho usaganize kuti Allah Ngwakuswa lonjezo Lake kwa atumiki Ake. Ndithu Allah ndi mwini mphamvu (salephera chilichonse), Ngobwezera chilango mwaukali
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek