×

Ndithudi iwo akonza chiwembu chawo ndipo chiwembu chawo chili ndi Mulungu ngakhale 14:46 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:46) ayat 46 in Chichewa

14:46 Surah Ibrahim ayat 46 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 46 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿وَقَدۡ مَكَرُواْ مَكۡرَهُمۡ وَعِندَ ٱللَّهِ مَكۡرُهُمۡ وَإِن كَانَ مَكۡرُهُمۡ لِتَزُولَ مِنۡهُ ٱلۡجِبَالُ ﴾
[إبراهِيم: 46]

Ndithudi iwo akonza chiwembu chawo ndipo chiwembu chawo chili ndi Mulungu ngakhale kuti chiwembu chawo chinali choti, chingathe kuchotsa mapiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقد مكروا مكرهم وعند الله مكرهم وإن كان مكرهم لتزول منه الجبال, باللغة نيانجا

﴿وقد مكروا مكرهم وعند الله مكرهم وإن كان مكرهم لتزول منه الجبال﴾ [إبراهِيم: 46]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, adachita ziwembu zawo, koma ziwembu zawo zili kwa Allah (akuzidziwa bwinobwino); ndipo ziwembu zawozo angakhale zitatha kuchotsetsa mapiri (sangamchite kanthu Mtumiki Muhammad (s.a.w} popeza Allah wamteteza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek