Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 7 - إبراهِيم - Page - Juz 13
﴿وَإِذۡ تَأَذَّنَ رَبُّكُمۡ لَئِن شَكَرۡتُمۡ لَأَزِيدَنَّكُمۡۖ وَلَئِن كَفَرۡتُمۡ إِنَّ عَذَابِي لَشَدِيدٞ ﴾
[إبراهِيم: 7]
﴿وإذ تأذن ربكم لئن شكرتم لأزيدنكم ولئن كفرتم إن عذابي لشديد﴾ [إبراهِيم: 7]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (kumbukani) pamene Mbuye wanu adalengeza kuti: “Ngati muthokoza, ndikuonjezerani; ndipo ngati simuthokoza (dziwani kuti) chilango changa nchaukali.” |