Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 8 - إبراهِيم - Page - Juz 13
﴿وَقَالَ مُوسَىٰٓ إِن تَكۡفُرُوٓاْ أَنتُمۡ وَمَن فِي ٱلۡأَرۡضِ جَمِيعٗا فَإِنَّ ٱللَّهَ لَغَنِيٌّ حَمِيدٌ ﴾
[إبراهِيم: 8]
﴿وقال موسى إن تكفروا أنتم ومن في الأرض جميعا فإن الله لغني﴾ [إبراهِيم: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Mûsa adati (kwa anthu ake): “Ngati inu mukana (pakusiya kuthokoza) pamodzi ndi onse a m’dziko, (Allah salabadira chilichonse pa zimenezo), ndithudi Allah Ngwachikwanekwane; Ngotamandidwa.” |