×

Kodi inu simunamve nkhani za anthu a Nowa, Aad, ndi Thamoud omwe 14:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:9) ayat 9 in Chichewa

14:9 Surah Ibrahim ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 9 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿أَلَمۡ يَأۡتِكُمۡ نَبَؤُاْ ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِكُمۡ قَوۡمِ نُوحٖ وَعَادٖ وَثَمُودَ وَٱلَّذِينَ مِنۢ بَعۡدِهِمۡ لَا يَعۡلَمُهُمۡ إِلَّا ٱللَّهُۚ جَآءَتۡهُمۡ رُسُلُهُم بِٱلۡبَيِّنَٰتِ فَرَدُّوٓاْ أَيۡدِيَهُمۡ فِيٓ أَفۡوَٰهِهِمۡ وَقَالُوٓاْ إِنَّا كَفَرۡنَا بِمَآ أُرۡسِلۡتُم بِهِۦ وَإِنَّا لَفِي شَكّٖ مِّمَّا تَدۡعُونَنَآ إِلَيۡهِ مُرِيبٖ ﴾
[إبراهِيم: 9]

Kodi inu simunamve nkhani za anthu a Nowa, Aad, ndi Thamoud omwe adalipo inu musanadze? Ndiponso za iwo amene adadza pambuyo pawo? Palibe adziwa za iwo kupatula Mulungu yekha. Atumwi awo adadza kwa iwo ndi zizindikiro zooneka koma iwo adatseka pakamwa pawo ndi manja awo ndipo adati, “Ndithudi ife sitikhulupirira mu zimene mwatumidwa, ndithudi ife tili ndi chikaiko pazimene mukutiitanira.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألم يأتكم نبأ الذين من قبلكم قوم نوح وعاد وثمود والذين من, باللغة نيانجا

﴿ألم يأتكم نبأ الذين من قبلكم قوم نوح وعاد وثمود والذين من﴾ [إبراهِيم: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi siidakudzereni nkhani ya omwe adalipo patsogolo panu? Anthu a Nuh, Âdi ndi Samudu? Ndi omwe adadza pambuyo pawo? Omwe palibe akuwadziwa kupatula Allah. Atumiki awo adawadzera ndi umboni oonekera. Koma adabwezera manja awo kukamwa kwawo (kusonyeza kutsutsa), ndipo adati: “Ndithu ife tikuzikana zimene mwatumizidwa nazo, ndipo ife tili mchikaiko pa zimene mukuitanira, ndiponso mchipeneko.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek