Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 14 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿وَلَوۡ فَتَحۡنَا عَلَيۡهِم بَابٗا مِّنَ ٱلسَّمَآءِ فَظَلُّواْ فِيهِ يَعۡرُجُونَ ﴾
[الحِجر: 14]
﴿ولو فتحنا عليهم بابا من السماء فظلوا فيه يعرجون﴾ [الحِجر: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tikadawatsekulira (awa osakhulupirira) khomo lakumwamba ndipo nkukhala akukwera m’menemo (ndi kutsika monga momwe amafunira kuti zimenezo zikhale chozizwitsa cha Mtumiki) |