Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 17 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿وَحَفِظۡنَٰهَا مِن كُلِّ شَيۡطَٰنٖ رَّجِيمٍ ﴾
[الحِجر: 17]
﴿وحفظناها من كل شيطان رجيم﴾ [الحِجر: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tidakuteteza kwa satana aliyense wopirikitsidwa (kumwambako akafuna kukamvetsera zimene zikunenedwa kumeneko) |