Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 20 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿وَجَعَلۡنَا لَكُمۡ فِيهَا مَعَٰيِشَ وَمَن لَّسۡتُمۡ لَهُۥ بِرَٰزِقِينَ ﴾
[الحِجر: 20]
﴿وجعلنا لكم فيها معايش ومن لستم له برازقين﴾ [الحِجر: 20]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo mmenemo takupangirani zinthu zoyendetsa moyo (wanu zakudya ndi zakumwa ndi zina zotere) ndiponso (tidakupatsani ana ndi ziweto) zomwe inu simungathe kuzidyetsa. (Ife ndife amene tikuzikonzera chakudya chawo, osati inu) |