Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 23 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿وَإِنَّا لَنَحۡنُ نُحۡيِۦ وَنُمِيتُ وَنَحۡنُ ٱلۡوَٰرِثُونَ ﴾
[الحِجر: 23]
﴿وإنا لنحن نحيي ونميت ونحن الوارثون﴾ [الحِجر: 23]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithudi, Ife ndife omwe timapereka moyo, ndi kupereka imfa. Ndiponso Ife ndi Amlowam’malo (a chinthu chilichonse chimene chikusiidwa chopanda mwini) |