Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 24 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿وَلَقَدۡ عَلِمۡنَا ٱلۡمُسۡتَقۡدِمِينَ مِنكُمۡ وَلَقَدۡ عَلِمۡنَا ٱلۡمُسۡتَـٔۡخِرِينَ ﴾
[الحِجر: 24]
﴿ولقد علمنا المستقدمين منكم ولقد علمنا المستأخرين﴾ [الحِجر: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu tikuwadziwa mwa inu amene atsogola (amene adafa kale), ndipo ndithu tikuwadziwanso amene atsalira (ali ndi moyobe ndi amene sanabadwe) |