Quran with Chichewa translation - Surah Al-hijr ayat 25 - الحِجر - Page - Juz 14
﴿وَإِنَّ رَبَّكَ هُوَ يَحۡشُرُهُمۡۚ إِنَّهُۥ حَكِيمٌ عَلِيمٞ ﴾ 
[الحِجر: 25]
﴿وإن ربك هو يحشرهم إنه حكيم عليم﴾ [الحِجر: 25]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu palibe chikaiko, Mbuye wako ndi Yemwe adzawasonkhanitsa (pambuyo pa imfa kuti adzawaweruze). Iye ndi Wanzeru zakuya, Wodziwa chilichonse |