Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 111 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿۞ يَوۡمَ تَأۡتِي كُلُّ نَفۡسٖ تُجَٰدِلُ عَن نَّفۡسِهَا وَتُوَفَّىٰ كُلُّ نَفۡسٖ مَّا عَمِلَتۡ وَهُمۡ لَا يُظۡلَمُونَ ﴾
[النَّحل: 111]
﴿يوم تأتي كل نفس تجادل عن نفسها وتوفى كل نفس ما عملت﴾ [النَّحل: 111]
Khaled Ibrahim Betala “(Akumbutse za) tsiku lomwe mzimu uliwonse udzadza ukudziteteza wokha (wosalabadira za mwana wake, mkazi wake ndi abale ake), ndipo mzimu uliwonse udzalipidwa molingana ndi zochita zake zimene unkachita, ndipo iwo sadzachitidwa chinyengo (pochepetsedwa mphoto yawo yoti alandire) |