×

Ndipo Iye adakhazikitsa mapiri padziko lapansi kuti lisagwedezeke pamodzi ndi inu, mitsinje 16:15 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:15) ayat 15 in Chichewa

16:15 Surah An-Nahl ayat 15 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 15 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَأَلۡقَىٰ فِي ٱلۡأَرۡضِ رَوَٰسِيَ أَن تَمِيدَ بِكُمۡ وَأَنۡهَٰرٗا وَسُبُلٗا لَّعَلَّكُمۡ تَهۡتَدُونَ ﴾
[النَّحل: 15]

Ndipo Iye adakhazikitsa mapiri padziko lapansi kuti lisagwedezeke pamodzi ndi inu, mitsinje ndi misewu kuti mutsogozedwe munjira zabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وألقى في الأرض رواسي أن تميد بكم وأنهارا وسبلا لعلكم تهتدون, باللغة نيانجا

﴿وألقى في الأرض رواسي أن تميد بكم وأنهارا وسبلا لعلكم تهتدون﴾ [النَّحل: 15]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo adaika panthaka mapiri ataliatali kuti (nthaka) isagwedezeke nanu; ndipo (adaika) mitsinje ndi misewu kuti muongoke (potsata njira yeniyeni ndikukafika komwe mukufuna)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek