Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 40 - النَّحل - Page - Juz 14
﴿إِنَّمَا قَوۡلُنَا لِشَيۡءٍ إِذَآ أَرَدۡنَٰهُ أَن نَّقُولَ لَهُۥ كُن فَيَكُونُ ﴾
[النَّحل: 40]
﴿إنما قولنا لشيء إذا أردناه أن نقول له كن فيكون﴾ [النَّحل: 40]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu liwu Lathu pa chinthu chimene tikuchifuna kuti chichitike ndikuchiuza basi kuti: “Chitika,” ndipo chimachitikadi |