×

Ndi zizindikiro zooneka ndiponso mabuku opatulika, Ife tavumbulutsa kwa iwe chikumbutso kuti 16:44 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:44) ayat 44 in Chichewa

16:44 Surah An-Nahl ayat 44 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 44 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿بِٱلۡبَيِّنَٰتِ وَٱلزُّبُرِۗ وَأَنزَلۡنَآ إِلَيۡكَ ٱلذِّكۡرَ لِتُبَيِّنَ لِلنَّاسِ مَا نُزِّلَ إِلَيۡهِمۡ وَلَعَلَّهُمۡ يَتَفَكَّرُونَ ﴾
[النَّحل: 44]

Ndi zizindikiro zooneka ndiponso mabuku opatulika, Ife tavumbulutsa kwa iwe chikumbutso kuti ulalikire anthu zonse zimene zatumizidwa kwa iwo ndi kuti akhoza kulingirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: بالبينات والزبر وأنـزلنا إليك الذكر لتبين للناس ما نـزل إليهم ولعلهم يتفكرون, باللغة نيانجا

﴿بالبينات والزبر وأنـزلنا إليك الذكر لتبين للناس ما نـزل إليهم ولعلهم يتفكرون﴾ [النَّحل: 44]

Khaled Ibrahim Betala
“(Tidabwera) ndi zisonyezo zoonekera pamodzi ndi mabuku; ndipo takuvumbulutsira ulaliki kuti uwafotokozere anthu zomwe zavumbulutsidwa kwa iwo kuti aganizire
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek