×

Kodi iwo amene amakonza chiwembu ndi odzikhulupirira kuti Mulungu sangawakwirire m’nthaka kapena 16:45 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:45) ayat 45 in Chichewa

16:45 Surah An-Nahl ayat 45 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 45 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿أَفَأَمِنَ ٱلَّذِينَ مَكَرُواْ ٱلسَّيِّـَٔاتِ أَن يَخۡسِفَ ٱللَّهُ بِهِمُ ٱلۡأَرۡضَ أَوۡ يَأۡتِيَهُمُ ٱلۡعَذَابُ مِنۡ حَيۡثُ لَا يَشۡعُرُونَ ﴾
[النَّحل: 45]

Kodi iwo amene amakonza chiwembu ndi odzikhulupirira kuti Mulungu sangawakwirire m’nthaka kapena kuti chilango sichingagwe pa iwo kuchokera ku mbali imene sali kuiyembekezera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أفأمن الذين مكروا السيئات أن يخسف الله بهم الأرض أو يأتيهم العذاب, باللغة نيانجا

﴿أفأمن الذين مكروا السيئات أن يخسف الله بهم الأرض أو يأتيهم العذاب﴾ [النَّحل: 45]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi adziika pachitetezo, amene akuchita ndale zoipa, kuti Allah sangawakwilire ndi nthaka, kapena chilango kuwadzera kuchokera komwe sadali kukudziwa (sadali kukuyembekezera)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek