×

Akadakhala kuti Mulungu anali kulanga anthu msanga chifukwa cha zoipa zawo, palibe 16:61 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:61) ayat 61 in Chichewa

16:61 Surah An-Nahl ayat 61 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 61 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿وَلَوۡ يُؤَاخِذُ ٱللَّهُ ٱلنَّاسَ بِظُلۡمِهِم مَّا تَرَكَ عَلَيۡهَا مِن دَآبَّةٖ وَلَٰكِن يُؤَخِّرُهُمۡ إِلَىٰٓ أَجَلٖ مُّسَمّٗىۖ فَإِذَا جَآءَ أَجَلُهُمۡ لَا يَسۡتَـٔۡخِرُونَ سَاعَةٗ وَلَا يَسۡتَقۡدِمُونَ ﴾
[النَّحل: 61]

Akadakhala kuti Mulungu anali kulanga anthu msanga chifukwa cha zoipa zawo, palibe cholengedwa ndi chimodzi chomwe chimene Iye akadachisiya ndi moyo. Koma Iye amawasunga mpaka tsiku lokhazikitsidwa, ndipo ngati nthawi yawo ikwana, ngakhale ndi kamphindi kochepa, iwo sangaichedwetse kapena kuifulumizitsa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولو يؤاخذ الله الناس بظلمهم ما ترك عليها من دابة ولكن يؤخرهم, باللغة نيانجا

﴿ولو يؤاخذ الله الناس بظلمهم ما ترك عليها من دابة ولكن يؤخرهم﴾ [النَّحل: 61]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek