×

“Ndipo idyani zipatso za mitundu yonse, ndipo yendani m’njira za Ambuye wanu 16:69 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nahl ⮕ (16:69) ayat 69 in Chichewa

16:69 Surah An-Nahl ayat 69 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nahl ayat 69 - النَّحل - Page - Juz 14

﴿ثُمَّ كُلِي مِن كُلِّ ٱلثَّمَرَٰتِ فَٱسۡلُكِي سُبُلَ رَبِّكِ ذُلُلٗاۚ يَخۡرُجُ مِنۢ بُطُونِهَا شَرَابٞ مُّخۡتَلِفٌ أَلۡوَٰنُهُۥ فِيهِ شِفَآءٞ لِّلنَّاسِۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَةٗ لِّقَوۡمٖ يَتَفَكَّرُونَ ﴾
[النَّحل: 69]

“Ndipo idyani zipatso za mitundu yonse, ndipo yendani m’njira za Ambuye wanu mosavutika.” Kuchokera m’mimba mwa njuchi, mumatuluka zakumwa zamitundu yosiyanasiyana ndipo m’menemo muli mankhwala ochiza anthu. Ndithudi mu izi muli zizindikiro kwa iwo amene amalingilira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ثم كلي من كل الثمرات فاسلكي سبل ربك ذللا يخرج من بطونها, باللغة نيانجا

﴿ثم كلي من كل الثمرات فاسلكي سبل ربك ذللا يخرج من بطونها﴾ [النَّحل: 69]

Khaled Ibrahim Betala
““Tsono idya zipatso zamtundu uliwonse ndikuyenda m’njira za Mbuye wako zimene wazifewetsa (kuziyenda).” Chimatuluka m’mimba mwake chakumwa cha utoto wosiyanasiyana (uchi), mwa icho muli kuchilitsa kwa anthu (kumatenda ochuluka), ndithu m’zimenezo muli zizindikiro kwa anthu oganiza (zinthu) mwakuya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek