×

Iye adati, “Ndithudi iwe uli kudziwa bwinobwino kuti zizindikiro izi sizinatumizidwe ndi 17:102 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:102) ayat 102 in Chichewa

17:102 Surah Al-Isra’ ayat 102 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 102 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿قَالَ لَقَدۡ عَلِمۡتَ مَآ أَنزَلَ هَٰٓؤُلَآءِ إِلَّا رَبُّ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ بَصَآئِرَ وَإِنِّي لَأَظُنُّكَ يَٰفِرۡعَوۡنُ مَثۡبُورٗا ﴾
[الإسرَاء: 102]

Iye adati, “Ndithudi iwe uli kudziwa bwinobwino kuti zizindikiro izi sizinatumizidwe ndi wina koma Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi ngati umboni wooneka ndi maso. Ndipo, ndithudi, ine ndiganiza kuti iwe, Farawo, ndiwe woonongeka.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال لقد علمت ما أنـزل هؤلاء إلا رب السموات والأرض بصائر وإني, باللغة نيانجا

﴿قال لقد علمت ما أنـزل هؤلاء إلا رب السموات والأرض بصائر وإني﴾ [الإسرَاء: 102]

Khaled Ibrahim Betala
“(Mûsa) adati: “Ndithu wadziwa kuti palibe amene watumiza (mitsutso) iyi kupatula Mbuye wathambo ndi nthaka kuti zikhale chiphanula maso. Koma ine ndikukuona iwe Farawo kuti waonongeka.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek