×

Ndipo musakhale oumira kapena opereka moononga chifukwa mungadzudzulidwe kapena kukhala osauka kwambiri 17:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:29) ayat 29 in Chichewa

17:29 Surah Al-Isra’ ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 29 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَلَا تَجۡعَلۡ يَدَكَ مَغۡلُولَةً إِلَىٰ عُنُقِكَ وَلَا تَبۡسُطۡهَا كُلَّ ٱلۡبَسۡطِ فَتَقۡعُدَ مَلُومٗا مَّحۡسُورًا ﴾
[الإسرَاء: 29]

Ndipo musakhale oumira kapena opereka moononga chifukwa mungadzudzulidwe kapena kukhala osauka kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولا تجعل يدك مغلولة إلى عنقك ولا تبسطها كل البسط فتقعد ملوما, باللغة نيانجا

﴿ولا تجعل يدك مغلولة إلى عنقك ولا تبسطها كل البسط فتقعد ملوما﴾ [الإسرَاء: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mkono wako usaukhalitse ngati kuti wamangidwa kukhosi kwako, ndiponso usautambasule mosayenera, ungadzakhale wodzudzulidwa ndiwosowa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek