×

Ili ndi gawo la luntha limene Ambuye wako wakuuza iwe. Ndipo usatumikire 17:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:39) ayat 39 in Chichewa

17:39 Surah Al-Isra’ ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 39 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿ذَٰلِكَ مِمَّآ أَوۡحَىٰٓ إِلَيۡكَ رَبُّكَ مِنَ ٱلۡحِكۡمَةِۗ وَلَا تَجۡعَلۡ مَعَ ٱللَّهِ إِلَٰهًا ءَاخَرَ فَتُلۡقَىٰ فِي جَهَنَّمَ مَلُومٗا مَّدۡحُورًا ﴾
[الإسرَاء: 39]

Ili ndi gawo la luntha limene Ambuye wako wakuuza iwe. Ndipo usatumikire mulungu wina kuonjezera pa Mulungu weniweni chifukwa mwina iwe ungaponyedwe ku Gahena, modzudzulidwa ndi mokankhidwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ذلك مما أوحى إليك ربك من الحكمة ولا تجعل مع الله إلها, باللغة نيانجا

﴿ذلك مما أوحى إليك ربك من الحكمة ولا تجعل مع الله إلها﴾ [الإسرَاء: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Izi ndi zina mwa za nzeru zomwe Mbuye wako wakuvumbulutsira. Usakhale ndi mulungu wina ndi kumphatikiza kwa Allah, kuti ungadzaponyedwe ku Jahannam uli wodzudzulidwa ndi wopirikitsidwa apa ndi apo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek