×

Auze akapolo anga kuti aziyankhula zokhazo zimene zili zabwino. Ndithudi Satana amafesa 17:53 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:53) ayat 53 in Chichewa

17:53 Surah Al-Isra’ ayat 53 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 53 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَقُل لِّعِبَادِي يَقُولُواْ ٱلَّتِي هِيَ أَحۡسَنُۚ إِنَّ ٱلشَّيۡطَٰنَ يَنزَغُ بَيۡنَهُمۡۚ إِنَّ ٱلشَّيۡطَٰنَ كَانَ لِلۡإِنسَٰنِ عَدُوّٗا مُّبِينٗا ﴾
[الإسرَاء: 53]

Auze akapolo anga kuti aziyankhula zokhazo zimene zili zabwino. Ndithudi Satana amafesa chidani pakati pawo. Ndithudi Satana, kwa munthu, ndi mdani woonekeratu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقل لعبادي يقولوا التي هي أحسن إن الشيطان ينـزغ بينهم إن الشيطان, باللغة نيانجا

﴿وقل لعبادي يقولوا التي هي أحسن إن الشيطان ينـزغ بينهم إن الشيطان﴾ [الإسرَاء: 53]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo auze akapolo Anga kuti (nthawi zonse) azinena zomwe zili zabwino; chifukwa satana amakhwirizira mikangano pakati pawo; ndithu satana kwa munthu, ndi m’dani woonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek