×

Ambuye wanu amadziwa kwambiri za inu ndipo ngati Iye afuna adzakuchitirani chifundo 17:54 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:54) ayat 54 in Chichewa

17:54 Surah Al-Isra’ ayat 54 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 54 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿رَّبُّكُمۡ أَعۡلَمُ بِكُمۡۖ إِن يَشَأۡ يَرۡحَمۡكُمۡ أَوۡ إِن يَشَأۡ يُعَذِّبۡكُمۡۚ وَمَآ أَرۡسَلۡنَٰكَ عَلَيۡهِمۡ وَكِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 54]

Ambuye wanu amadziwa kwambiri za inu ndipo ngati Iye afuna adzakuchitirani chifundo kapena ngati Iye afuna adzakulangani. Ndipo Ife sitidakutumize iwe kuti ukhale wowayang’anira iwo ayi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ربكم أعلم بكم إن يشأ يرحمكم أو إن يشأ يعذبكم وما أرسلناك, باللغة نيانجا

﴿ربكم أعلم بكم إن يشأ يرحمكم أو إن يشأ يعذبكم وما أرسلناك﴾ [الإسرَاء: 54]

Khaled Ibrahim Betala
“Mbuye wanu akukudziwani bwino. Ngati afuna akuchitirani chisoni (mukatembenukira kwa Iye), ndipo ngati afuna, akulangani (mukapitiriza kumnyoza); ndipo sitidakutumize kuti ukhale muyang’anili wawo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek