×

Kodi inu muli ndi chikhulupiriro chakuti Iye sangakumizeni m’dera lililonse la pamtunda 17:68 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:68) ayat 68 in Chichewa

17:68 Surah Al-Isra’ ayat 68 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 68 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿أَفَأَمِنتُمۡ أَن يَخۡسِفَ بِكُمۡ جَانِبَ ٱلۡبَرِّ أَوۡ يُرۡسِلَ عَلَيۡكُمۡ حَاصِبٗا ثُمَّ لَا تَجِدُواْ لَكُمۡ وَكِيلًا ﴾
[الإسرَاء: 68]

Kodi inu muli ndi chikhulupiriro chakuti Iye sangakumizeni m’dera lililonse la pamtunda kapena kuti sangakutumizireni mphepo yamkuntho? Pamenepo inu simudzapeza wina aliyense wokuthandizani

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أفأمنتم أن يخسف بكم جانب البر أو يرسل عليكم حاصبا ثم لا, باللغة نيانجا

﴿أفأمنتم أن يخسف بكم جانب البر أو يرسل عليكم حاصبا ثم لا﴾ [الإسرَاء: 68]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi mukudziika pa chitetezo ndi chilango cha Allah (mukafika pa ntunda) kuti Allah sangakulowetseni pansi mbali iliyonse ya pa ntunda, kapena sangakutumizireni chigumula chamchenga (kapena miyala) kenako inu simudzapeza mtetezi (wokupulumutsani ku chilangocho)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek