×

Kapena inu mukukhulupirira kuti sangakubwezereninso m’nyanjamo kachiwiri ndi kukutumizirani mphepo yamkuntho, ndikukumizani 17:69 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:69) ayat 69 in Chichewa

17:69 Surah Al-Isra’ ayat 69 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 69 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿أَمۡ أَمِنتُمۡ أَن يُعِيدَكُمۡ فِيهِ تَارَةً أُخۡرَىٰ فَيُرۡسِلَ عَلَيۡكُمۡ قَاصِفٗا مِّنَ ٱلرِّيحِ فَيُغۡرِقَكُم بِمَا كَفَرۡتُمۡ ثُمَّ لَا تَجِدُواْ لَكُمۡ عَلَيۡنَا بِهِۦ تَبِيعٗا ﴾
[الإسرَاء: 69]

Kapena inu mukukhulupirira kuti sangakubwezereninso m’nyanjamo kachiwiri ndi kukutumizirani mphepo yamkuntho, ndikukumizani chifukwa chakusakhulupirira kwanu ndipo kuti inu simudzapeza wokuthandizani polimbana ndi Ife

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أم أمنتم أن يعيدكم فيه تارة أخرى فيرسل عليكم قاصفا من الريح, باللغة نيانجا

﴿أم أمنتم أن يعيدكم فيه تارة أخرى فيرسل عليكم قاصفا من الريح﴾ [الإسرَاء: 69]

Khaled Ibrahim Betala
“Kapena mwadziika pachitetezo kuti (Allah) sadzakubwezeraninso m’nyanjamo kachiwiri ndipo nkudzakutumizirani chimphepo chaukali ndikukumizani chifukwa cha kusakhulupirira (ndi kusathokoza kwanu,) kenako inu nkusapeza wokutetezani kwa Ife
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek