×

Ndithudi Ife tawalemekeza ana a Adamu, ndipo Ife tawanyamula pamtunda ndi pa 17:70 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:70) ayat 70 in Chichewa

17:70 Surah Al-Isra’ ayat 70 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 70 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿۞ وَلَقَدۡ كَرَّمۡنَا بَنِيٓ ءَادَمَ وَحَمَلۡنَٰهُمۡ فِي ٱلۡبَرِّ وَٱلۡبَحۡرِ وَرَزَقۡنَٰهُم مِّنَ ٱلطَّيِّبَٰتِ وَفَضَّلۡنَٰهُمۡ عَلَىٰ كَثِيرٖ مِّمَّنۡ خَلَقۡنَا تَفۡضِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 70]

Ndithudi Ife tawalemekeza ana a Adamu, ndipo Ife tawanyamula pamtunda ndi pa nyanja ndipo tawapatsa zinthu zabwino ndiponso tawalemekeza kuposa zina zimene talenga ndi ulemu wapadera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد كرمنا بني آدم وحملناهم في البر والبحر ورزقناهم من الطيبات وفضلناهم, باللغة نيانجا

﴿ولقد كرمنا بني آدم وحملناهم في البر والبحر ورزقناهم من الطيبات وفضلناهم﴾ [الإسرَاء: 70]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu tawalemekeza ana a Adam; ndipo tawapatsa zokwera pa ntunda ndi pa nyanja; tawapatsa zopatsa zabwino kwambiri; ndipo tawapatsa ulemelero kuposa zambiri m’zomwe tidalenga; ulemelero waukulu kwabasi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek