×

Koma iye amene ali wakhungu m’moyo uno adzakhalanso wakhungu m’moyo umene uli 17:72 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:72) ayat 72 in Chichewa

17:72 Surah Al-Isra’ ayat 72 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 72 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَمَن كَانَ فِي هَٰذِهِۦٓ أَعۡمَىٰ فَهُوَ فِي ٱلۡأٓخِرَةِ أَعۡمَىٰ وَأَضَلُّ سَبِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 72]

Koma iye amene ali wakhungu m’moyo uno adzakhalanso wakhungu m’moyo umene uli nkudza ndipo adzasochera kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن كان في هذه أعمى فهو في الآخرة أعمى وأضل سبيلا, باللغة نيانجا

﴿ومن كان في هذه أعمى فهو في الآخرة أعمى وأضل سبيلا﴾ [الإسرَاء: 72]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene ali wakhungu pano (pa dziko lapansi posapenya zizindikiro) adzakhalanso wakhungu pa tsiku la chimaliziro, ndipo adzakhala wosokera kwambiri njira (kumeneko)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek