×

Ndithudi adatsala pang’ono kukuchititsa mantha m’dziko ndi cholinga choti akuchotse m’menemo. Zikadatheka 17:76 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:76) ayat 76 in Chichewa

17:76 Surah Al-Isra’ ayat 76 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 76 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَإِن كَادُواْ لَيَسۡتَفِزُّونَكَ مِنَ ٱلۡأَرۡضِ لِيُخۡرِجُوكَ مِنۡهَاۖ وَإِذٗا لَّا يَلۡبَثُونَ خِلَٰفَكَ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[الإسرَاء: 76]

Ndithudi adatsala pang’ono kukuchititsa mantha m’dziko ndi cholinga choti akuchotse m’menemo. Zikadatheka kutero iwo sakadakhala pambuyo pako, koma kwa kanthawi kochepa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإن كادوا ليستفزونك من الأرض ليخرجوك منها وإذا لا يلبثون خلافك إلا, باللغة نيانجا

﴿وإن كادوا ليستفزونك من الأرض ليخرجوك منها وإذا لا يلبثون خلافك إلا﴾ [الإسرَاء: 76]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo padatsala pang’ono kuti akusowetse mtendere m’dziko ili (la Makka) kuti akutulutse m’menemo; koma pambuyo pako sakadakhala (ndi moyo) kupatula (nthawi) yochepa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek