×

Nena, “Ambuye ndilowetseni kulowa kwa bwino ndipo nditulutseni mwaubwino. Ndipo ndipatseni kuchokera 17:80 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:80) ayat 80 in Chichewa

17:80 Surah Al-Isra’ ayat 80 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 80 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَقُل رَّبِّ أَدۡخِلۡنِي مُدۡخَلَ صِدۡقٖ وَأَخۡرِجۡنِي مُخۡرَجَ صِدۡقٖ وَٱجۡعَل لِّي مِن لَّدُنكَ سُلۡطَٰنٗا نَّصِيرٗا ﴾
[الإسرَاء: 80]

Nena, “Ambuye ndilowetseni kulowa kwa bwino ndipo nditulutseni mwaubwino. Ndipo ndipatseni kuchokera kwa Inu mphamvu yondithandiza.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقل رب أدخلني مدخل صدق وأخرجني مخرج صدق واجعل لي من لدنك, باللغة نيانجا

﴿وقل رب أدخلني مدخل صدق وأخرجني مخرج صدق واجعل لي من لدنك﴾ [الإسرَاء: 80]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo nena (mawu awa pomwe ukupemphera): “Mbuye wanga! Ndilowetseni, kulowetsa kwabwino (paliponse pamene ndikulowa), ndiponso nditulutseni, kutulutsa kwabwino (paliponse pamene ndikutuluka); ndipatseni mphamvu zochokera kwa Inu zondithandiza ndi kugonjetsera adani.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek