×

Ndipo titumiza kuchokera m’Korani mankhwala ochiza ndiponso chisoni kwa onse okhulupirira, ndipo 17:82 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:82) ayat 82 in Chichewa

17:82 Surah Al-Isra’ ayat 82 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 82 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَنُنَزِّلُ مِنَ ٱلۡقُرۡءَانِ مَا هُوَ شِفَآءٞ وَرَحۡمَةٞ لِّلۡمُؤۡمِنِينَ وَلَا يَزِيدُ ٱلظَّٰلِمِينَ إِلَّا خَسَارٗا ﴾
[الإسرَاء: 82]

Ndipo titumiza kuchokera m’Korani mankhwala ochiza ndiponso chisoni kwa onse okhulupirira, ndipo imaonjezera kwa anthu osakhulupirira chionongeko

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وننـزل من القرآن ما هو شفاء ورحمة للمؤمنين ولا يزيد الظالمين إلا, باللغة نيانجا

﴿وننـزل من القرآن ما هو شفاء ورحمة للمؤمنين ولا يزيد الظالمين إلا﴾ [الإسرَاء: 82]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tikuivumbulutsa Qur’an yomwe imachiritsa (matenda a mmitima) ndiponso ndi chifundo kwa okhulupirira. Komabe osalungama siikuwaonjezera (kanthu kena) koma kutayika
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek